By Durell Namasani
Malawians have taken to Social Media to react on a new song titled “Moyo Wina” by legendary musician Lulu and Afro-pop star Kell Kay with majority of them blasting the two forΒ what they are describing as a poor quality song.
Apart from Kell Kay, the song also features the Kambwiri Sisters on the backing vocals.
Below are some of the comments on various social media platforms.
Grant Tiwope Chiwalo
“Lulu produced the song himself koma Nde Zidazo plus voice chimphwilikiti kkkk. Tricky beats Ali kuti? If you are an artist and umadziwa production probability yopala ku production ku nyimbo yako imakhala high. Ndi bwino kumapeza ena akuthandizile, production iyiyi likanakhala kale lija mukuimba ku malembe tikanati mwaphaaa koma Panopa zinthu zinasintha let’s accept.
Nyimboyo ndi ya bhoo koma production yo ngat ya beginner.”
Ron CZ Zeleza
“I hope artists check these comments.. for future releases.coz eh.”
Victor Daffrece
“Nyimbo ngati kuti amathamangira kuipanga master kuopa kuti ma units amagetsi atha kuthera panjiraπ¬π¬.”
Annie White
“Nyimbo yabho koma too much noise aaaaa Lulu you can do better. tamapitani ma studio olongosoka. iwetu ma size ako ndi achina Lawi mukajambulenso nyimboyi.”
Mayamiko Demo
“A good song. But the production sounds muddy. Maybe my gadget has a problemπ.”
Chifundo Nserebo
“If this is the original song then… I guess they need to go back to studio… I don’t if it’s only me… But honestly I can’t here anything even if I try to put on headphones…
Shame πππππ.”
Joe Zephy Mbundungu
“Why can’t I hear anything the engineer of this song did not do a good Job send the Stems tigwile ntchito π
.”
Michelle Moir
“Why canβt I hear anything? Who produced this song abale musandiyipitsire ma artist anga okondeka asaaaah what is this? Lulu and Kell Kay please redo the song and let someone else produce it! Muli phokoso abale nyimboyi sikumveka bwino.”
Eddie Malikita
“Eeeeh tune km iyi π₯π₯π₯π₯
Special honour to Ching’aning’ani maΒ backing vocals achabe fadha ππππ.”
Bright Bentonie Mzoma
“The Lulu we have known is now back after some time. Good piece.”
G Saukile Jnr
“Iyiyi ndye mwapha guys back vocals yo eish ngat akumenya nd angelo kumwamba tuπ₯π₯π₯π₯
Official audio ili kuti kma tipeze ya pa repeat Friday li.”
Leo Khumalo
“Beat yopanda olo touch olooo mh. Nde kuona ma lyrics akeo achimwanatu and osamphanaπ¨βπ¦― mpaka kell kay kukudya koma nonse mutaviika π.”
Du Fu
“Palibe chikumveka chanzeru pa nyimbo yo ingosokosa basi “
Lawrence Nyando
“Kunena chilungamo iyiyi nde zero.ghetto yakana. Tinene kuti yawakanika. Tikubwera Kaye Handede komaso Awo.”
Raphy Man Zuze
“Mbola man joy
Apala akungoyimba ngat Wana bolaso Kell Kay wayeserakoππππππ.”
Seth J Muheku
“Munthu wamkulu akapala kulankhula kwake zimavuta bwanjiπ₯± ndingotumiza vn kma…ππ.”
You can watch the brand new song by following the link below