Chimwendo adzudzula Chipani Cha DPP polankhula Mawu odzetsa mantha pakati pa anthu
Mlembi wamkulu wachipani cha Malawi Congress (MCP), a Richard Chimwendo Banda, wadzuduzula zimene akuchita atsogoleri ena achipani cha Democratic Progressive (DPP) pomalankhula mawu odzetsa mpungwepungwe komanso mantha pakati pa anthu…