Amangidwa kaamba kobela anthu powanamiza kuti awapezera ntchito kuchipatala
Olemba: Sylvester Chibwana Apolisi ku Lilongwe akusunga mchitokosi amayi awiri ogwira ntchito zachipatala amene akuwaganizira kuti anabera anthu ndalama yokwana K600 000 powanamiza kuti awathandiza kupeza ntchito kuchipatala. Malingana ndi…