Chakwera apeza ndalama zomangira likulu la ntchito za mabwalo
Wolemba: Linda Kwanjana Boma la Malawi ndi boma la China lachiwili pa 4 September, 2024 lasaina mgwirizano wa ndalama pafupifupi MK50 billion zomwe zithandizile pa ntchito yomanga likulu la ntchito…