A Ken Zikhale Ng’oma amema anthu akalembetse mu kaundula
By Staff Reporter Hon Zikhale Ng’oma akupitiliza ntchito yomemeza anthu kuti akalembetse mwaunyinji mu kaundula wa voti pomwe lero ali Ku Usiska Ku Nkhata-bay North Constituency. Pa ulendowu,a Zikhale akuyenda…