Rev Kamuyambeni ndi A Samson Mithenga akana malipoti oti alowa UTM
Wolemba Mtolankhani Wathu Mamembala a chipani cha Malawi Congress (MCP) m’busa Mwai Kamuyambeni komanso a Samson Nthenga atsutsa malipoti oti alowa chipani cha UTM. Izi zikutsatira chithunzi chomwe awiriwa anajambulitsa…