A Zikhale afunila zabwino Nduna Yatsopano Vitumbiko Mumba
Wolemba: Mtolankhani Wathu Nduna yazachitetezo cha mdziko lino Dr. Ken Zikhale Reeves Ng’oma ayamikira a Vitumbiko Mumba posankhidwa kukhala nduna ya za ntchito. A Ng’oma ati kusankhidwa kwa a Mumba…